-
Deuteronomo 8:17, 18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ngati mumtima mwanu munganene kuti, ‘Chuma ichi ndachipeza chifukwa cha ntchito ya manja anga komanso mphamvu zanga,’+ 18 muzikumbukira kuti ndi Yehova Mulungu wanu amene amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbira kwa makolo anu, ngati mmene zilili lero.+
-
-
Miyambo 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chuma cha munthu wolemera chili ngati mzinda wokhala ndi mpanda wolimba.
Ndipo mʼmaganizo mwake chili ngati mpanda umene ukumuteteza.+
-