Mlaliki 8:2, 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikunena kuti: “Uzimvera malamulo a mfumu+ polemekeza lumbiro limene unachita kwa Mulungu.+ 3 Usafulumire kuchoka pamaso pake,+ ndipo usayambe kuchita nawo zinthu zoipa.+ Chifukwa mfumuyo ikhoza kuchita chilichonse chimene ikufuna kuchita,
2 Ndikunena kuti: “Uzimvera malamulo a mfumu+ polemekeza lumbiro limene unachita kwa Mulungu.+ 3 Usafulumire kuchoka pamaso pake,+ ndipo usayambe kuchita nawo zinthu zoipa.+ Chifukwa mfumuyo ikhoza kuchita chilichonse chimene ikufuna kuchita,