-
1 Mafumu 12:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Koma mfumuyo inayankha anthuwo mwaukali ndipo sinamvere malangizo a anthu achikulire* aja. 14 Inayankha anthuwo motsatira malangizo a achinyamata aja. Inati: “Bambo anga anakusenzetsani goli lolemera koma ineyo ndiwonjezera goli lanulo. Bambo anga ankakukwapulani ndi zikwapu koma ineyo ndizikukwapulani ndi zikoti zaminga.”
-