-
Salimo 64:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndibiseni ku ziwembu zachinsinsi za anthu oipa,+
Kwa gulu la anthu ochita zoipa.
-
-
Salimo 64:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Adzawonongedwa chifukwa cha zolankhula za lilime lawo lomwe,+
Onse amene adzaone zimenezi adzapukusa mitu yawo.
-