-
Mlaliki 6:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndi ndani akudziwa zinthu zabwino zimene munthu angachite pa masiku ochepa a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Chifukwa ndi ndani angauze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?
-