Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mbiri 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo anthu osowa zochita ndi opanda pake anakhala kumbali yake. Iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu mwana wa Solomo chifukwa Rehobowamuyo anali wamngʼono komanso wamantha ndipo sakanatha kulimbana nawo.

  • 2 Mbiri 36:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehoyakini+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 18 ndipo analamulira miyezi itatu ndi masiku 10 ku Yerusalemu. Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani