Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Miyambo 21:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zinthu zimene munthu waulesi amalakalaka zidzamupha,

      Chifukwa manja ake amakana kugwira ntchito.+

  • Miyambo 24:33, 34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ukapitiriza kugona pangʼono, ukapitiriza katulo pangʼono,

      Ukapitiriza kupinda manja pangʼono kuti upume,

      34 Umphawi wako udzabwera ngati wachifwamba,

      Ndipo kusauka kwako kudzabwera ngati munthu wokhala ndi zida.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani