-
Nyimbo ya Solomo 4:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Uli ngati munda* wa mitengo imene nthambi zake zili ndi makangaza ambiri
Umene uli ndi zipatso zabwino kwambiri, maluwa a hena ndi mitengo ya nado,
-