-
Nyimbo ya Solomo 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 “Ndiwe wokongola wokondedwa wanga.
Ndiwe chiphadzuwa.
Maso ako ali ngati maso a njiwa munsalu yako yophimba kumutuyo.
Tsitsi lako lili ngati gulu la mbuzi
Zimene zikuthamanga potsika mapiri a ku Giliyadi.+
-