Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Samueli 30:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno anapeza munthu wina wa ku Iguputo patchire. Anamutenga nʼkupita naye kwa Davide ndipo anamupatsa chakudya ndi madzi akumwa. 12 Anamupatsanso keke ya nkhuyu zouma ndi makeke awiri a mphesa zouma. Atadya anapeza mphamvu, chifukwa anakhala osadya chakudya kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, masana ndi usiku.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani