-
Nyimbo ya Solomo 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndakulumbiritsani inu ana aakazi a ku Yerusalemu,
Pali insa ndiponso pali mphoyo zakutchire kuti:
Musayese kudzutsa chikondi mwa ine nthawi yake isanakwane.”+
-
-
Nyimbo ya Solomo 8:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndakulumbiritsani inu ana aakazi a ku Yerusalemu kuti:
Musayese kudzutsa chikondi mwa ine nthawi yake isanakwane.”+
-