Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Nyimbo ya Solomo 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 “Panopa ndili mʼtulo koma mtima wanga uli maso.+

      Ndikumva wachikondi wanga akugogoda.”

      “Nditsegulire iwe mchemwali wanga, wokondedwa wanga,

      Njiwa yanga, iwe wopanda chilema.

      Chifukwa mutu wanga wanyowa ndi mame,

      Tsitsi langa lopotanapotana, lanyowa ndi chinyezi cha usiku.”+

  • Yeremiya 48:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Inu anthu okhala ku Mowabu, chokani mʼmizinda ndipo mukakhale pathanthwe.

      Mukhale ngati njiwa imene imamanga chisa chake mʼmbali mwa khomo la phanga.’”

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani