-
Nyimbo ya Solomo 2:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Wachikondi wanga ali ngati insa komanso mphoyo yaingʼono.+
Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma la nyumba yathu.
Akuyangʼana mʼmawindo,
Akusuzumira pazotchingira mʼmawindo.
-
-
Nyimbo ya Solomo 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 “Fulumira wachikondi wanga,
Thamanga ngati insa+
Kapena ngati mphoyo yaingʼono
Pamapiri amaluwa onunkhira.”
-