Salimo 120:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsoka kwa ine, chifukwa ndakhala mʼdziko la Meseki+ ngati mlendo. Ndimakhala mutenti pakati pa matenti a ku Kedara.+ Ezekieli 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Unalemba ntchito Aluya ndi atsogoleri onse a ku Kedara,+ amene ankagulitsa ana a nkhosa, nkhosa zamphongo ndi mbuzi.+
5 Tsoka kwa ine, chifukwa ndakhala mʼdziko la Meseki+ ngati mlendo. Ndimakhala mutenti pakati pa matenti a ku Kedara.+
21 Unalemba ntchito Aluya ndi atsogoleri onse a ku Kedara,+ amene ankagulitsa ana a nkhosa, nkhosa zamphongo ndi mbuzi.+