Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Nehemiya 3:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Palali mwana wa Uzai, anakonza mpandawo kutsogolo kwa khoma lothandizira kuti mpanda usagwe. Anakonzanso nsanja yochokera pa Nyumba ya Mfumu+ imene ili kumtunda mʼBwalo la Alonda.+ Pedaya mwana wa Parosi, anapitiriza kuchokera pamene Palali+ analekezera.

  • Nyimbo ya Solomo 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Khosi lako+ lili ngati nsanja ya mnyanga wa njovu.+

      Maso ako+ ali ngati madamu a madzi a ku Hesiboni,+

      Amene ali pafupi ndi geti la Bati-rabimu.

      Mphuno yako ili ngati nsanja ya ku Lebanoni,

      Imene inayangʼana cha ku Damasiko.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani