Nyimbo ya Solomo 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tiye tilawirire mʼmamawa tipite kuminda ya mpesa.Tikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira,Ngati maluwa amasula+Ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+ Kumeneko ndikakusonyeza chikondi changa.+
12 Tiye tilawirire mʼmamawa tipite kuminda ya mpesa.Tikaone ngati mitengo ya mpesa yaphukira,Ngati maluwa amasula+Ngati mitengo ya makangaza yachita maluwa.+ Kumeneko ndikakusonyeza chikondi changa.+