Nyimbo ya Solomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Wokondedwa wangawe,+ ndiwe wokongola ngati Tiriza,*+Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+Ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera.+
4 “Wokondedwa wangawe,+ ndiwe wokongola ngati Tiriza,*+Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+Ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera.+