-
Esitere 2:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mtsikana aliyense ankakhala ndi nthawi yake yokaonekera kwa Mfumu Ahasiwero akamaliza kumuchitira zonse zimene amayenera kuwachitira akazi pa miyezi 12. Atsikanawo ankawapaka mafuta a mule*+ miyezi 6 kenako nʼkuwapakanso mafuta a basamu+ pamodzi ndi mafuta enanso okongoletsa miyezi inanso 6. Akachita zimenezi ankakhala kuti amaliza dongosolo lonse lowakongoletsera.
-
-
Nyimbo ya Solomo 4:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “Mpaka kunja kutayamba kuwomba kamphepo kayaziyazi ndiponso mpaka mithunzi itachoka,
Ndipita kuphiri la mule
Ndiponso kuzitunda za lubani.”+
-