-
Yesaya 35:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Deralo lidzachitadi maluwa.+
Lidzasangalala ndipo lidzafuula chifukwa cha chisangalalo.
Anthu adzaona ulemerero wa Yehova ndi kukongola kwa Mulungu wathu.
-