Nyimbo ya Solomo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Wachikondi wanga ndi wanga, ndipo ine ndine wake.+ Iye akudyetsa ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.+ Nyimbo ya Solomo 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wachikondi wanga, ine ndi wakeNdipo iye ndi wanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu umene uli pakati pa maluwa.”+
16 “Wachikondi wanga ndi wanga, ndipo ine ndine wake.+ Iye akudyetsa ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa.+
3 Wachikondi wanga, ine ndi wakeNdipo iye ndi wanga.+ Iye akudyetsera ziweto msipu umene uli pakati pa maluwa.”+