-
Mika 1:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Muchotse tsitsi lonse ndipo mumete mpala chifukwa cha ana anu amene mumawakonda.
Metani mpala ngati wa chiwombankhanga,
Chifukwa chakuti ana anuwo atengedwa kupita kudziko lina.”+
-