Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezara 1:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yesaya 41:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ine ndapatsa mphamvu winawake kuchokera kumpoto, ndipo abwera.+

      Iye adzachokera kotulukira dzuwa*+ ndipo adzaitana pa dzina langa.

      Adzapondaponda olamulira* ngati akuponda dongo+

      Ngati woumba amene amapondaponda dongo laliwisi.

  • Yesaya 45:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yesaya 46:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Danieli 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wa Mfumu Koresi+ ya Perisiya, Mulungu anamuululira nkhani inayake Danieli, amene ankadziwikanso ndi dzina lakuti Belitesazara.+ Nkhani imene anauzidwayo inali yoona ndipo inali yokhudza nkhondo yaikulu. Danieli anamvetsa nkhani imeneyi ndipo anathandizidwa kumvetsa zinthu zimene anaonazo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani