-
1 Mafumu 21:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, anauza Ahabu kuti: “Pitani mukatenge munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, chifukwa Naboti panopa wafa.” 16 Ahabu atangomva kuti Naboti wafa, anapita kukatenga munda wa mpesa wa Naboti wa ku Yezereeli kuti ukhale wake.
-