Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mafumu 25:18-21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+ 19 Mumzindawo anatengamonso nduna imodzi yapanyumba ya mfumu imene inkayangʼanira asilikali. Anatenganso anzake 5 a mfumu amene anawapeza mumzindawo. Komanso anatenga mlembi wa mkulu wa asilikali yemwe ankasonkhanitsa anthu ndiponso amuna 60 mwa anthu wamba amene anawapeza mumzindawo. 20 Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthuwa nʼkupita nawo ku Ribila kwa mfumu ya Babulo.+ 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila mʼdziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+

  • Salimo 137:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+

      Wosangalala adzakhala amene adzakubwezere

      Zimene iwe watichitira.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani