-
Miyambo 31:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Nʼkosayenera kuti mafumu azimwa vinyo,
Nʼkosayenera kuti mafumu azichita zimenezi, iwe Lemueli,
Kapena kuti olamulira azinena kuti: “Kodi chakumwa changa chili kuti?”+
5 Chifukwa angamwe nʼkuiwala malamulo
Ndiponso kupondereza ufulu wa anthu onyozeka.
-