Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 31:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndikadzawalowetsa mʼdziko limene ndinalumbira kwa makolo awo,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo akadzadya nʼkukhuta, zinthu nʼkuyamba kuwayendera bwino,*+ adzatembenukira kwa milungu ina nʼkuyamba kuitumikira. Iwo adzandichitira mwano komanso kuphwanya pangano langa.+

  • 2 Mafumu 17:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Nehemiya 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Koma iwo anali osamvera ndipo anakugalukirani.+ Anasiya kutsatira Chilamulo chanu, anapha aneneri anu amene ankawachenjeza kuti abwerere kwa inu ndipo anachita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+

  • Yesaya 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+

      Anthu olemedwa ndi zolakwa,

      Ana a anthu ochita zoipa, ana a makhalidwe oipa.

      Iwo asiya Yehova.+

      Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu.

      Iwo atembenuka nʼkumusiya.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani