2 Mafumu 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nehemiya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anandiyankha kuti: “Anthu amene anatsala mʼchigawo,* omwe anapulumuka ku ukapolo, ali pamavuto aakulu ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda wa Yerusalemu unagwa+ ndipo mageti ake anatenthedwa ndi moto.”+
3 Iwo anandiyankha kuti: “Anthu amene anatsala mʼchigawo,* omwe anapulumuka ku ukapolo, ali pamavuto aakulu ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda wa Yerusalemu unagwa+ ndipo mageti ake anatenthedwa ndi moto.”+