Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 26:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mizinda yanu ndidzaiwononga+ ndi lupanga ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu, komanso sindidzalandira nsembe zanu za kafungo kosangalatsa.*

  • Yesaya 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova wanena kuti: “Kodi nsembe zanu zambirimbirizo zili ndi phindu lanji kwa ine?+

      Nsembe zanu zopsereza za nkhosa zamphongo+ ndiponso mafuta a nyama zodyetsedwa bwino+ zandikwana.

      Sindikusangalala ndi magazi+ a ngʼombe zazingʼono zamphongo,+ a ana a nkhosa ndiponso magazi a mbuzi.+

  • Yeremiya 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako Yehova anandiuza kuti: “Ngakhale Mose ndi Samueli akanaima pamaso panga,+ anthu awa sindikanawakomera mtima. Achotse pamaso panga. Asiye apite.

  • Ezekieli 24:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 ‘Ndiwe wodetsedwa chifukwa cha khalidwe lako lonyansa.+ Ine ndinayesa kukuyeretsa, koma sunayere chifukwa zonyansa zako sizinachoke. Sudzayera mpaka mkwiyo wanga utatha.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani