2 Mbiri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zinali choncho chifukwa zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko. Ezekieli 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Sitima zapamadzi za ku Tarisi+ zinkanyamula katundu wako wamalonda,Choncho unali ndi chuma chambiri ndipo unalemera* pakati pa nyanja.
21 Zinali choncho chifukwa zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko.
25 Sitima zapamadzi za ku Tarisi+ zinkanyamula katundu wako wamalonda,Choncho unali ndi chuma chambiri ndipo unalemera* pakati pa nyanja.