-
Yeremiya 9:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 “Aliyense asamale ndi mnzake,
Ndipo musamakhulupirire ngakhale mʼbale wanu.
5 Aliyense amapusitsa mnzake,
Ndipo palibe amene amalankhula zoona.
Aphunzitsa lilime lawo kulankhula chinyengo.+
Iwo amadzitopetsa okha pochita zinthu zoipa.
-