Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mbiri 33:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Manase+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 12 ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+

  • 2 Mbiri 33:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Manase anatentha* ana ake aamuna pamoto+ mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu,+ ankachita zamatsenga,+ ankawombeza, ankachita zanyanga ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu ndi olosera zamʼtsogolo.+ Iye anachita zinthu zoipa kwambiri pamaso pa Yehova ndipo anamukwiyitsa.

  • Ezekieli 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iye anandiyankha kuti: “Zolakwa za nyumba ya Isiraeli ndi Yuda nʼzazikulu kwambiri.+ Dziko lawo ladzaza ndi kukhetsa magazi+ ndipo mumzindamo mwadzaza zinthu zopanda chilungamo.+ Iwo akunena kuti, ‘Yehova wachokamo mʼdziko muno ndipo Yehova sakuona.’+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani