-
2 Mbiri 32:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Zimenezi zitachitika, anthu ambiri ankabweretsa mphatso kwa Yehova ku Yerusalemu ndi zinthu zabwino kwambiri kwa Hezekiya mfumu ya Yuda,+ moti iye ankalemekezedwa ndi anthu a mitundu yonse.
-