2 Koma mumadana ndi zinthu zabwino+ ndipo mumakonda zinthu zoipa.+
Mumasenda khungu la anthu anga nʼkuchotsa mnofu pamafupa awo.+
3 Mumadyanso mnofu wa anthu anga,+
Ndipo mumasenda khungu lawo.
Mumaswa mafupa awo nʼkuwaphwanyaphwanya.+
Ngati zinthu zimene zaphikidwa mumphika komanso ngati nyama imene ili mumphika.