2 Mafumu 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+ Danieli 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Shadireki,* Misheki* ndi Abedinego+ kuti akhale oyangʼanira ntchito za boma mʼchigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli ankagwira ntchito kunyumba ya mfumu. Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+
49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Shadireki,* Misheki* ndi Abedinego+ kuti akhale oyangʼanira ntchito za boma mʼchigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli ankagwira ntchito kunyumba ya mfumu.