-
Oweruza 8:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndolo zapamphuno zagolide zimene anamupatsa zinali zolemera masekeli* agolide 1,700, osawerengera zokongoletsa zooneka ngati mwezi, zovala mʼkhosi komanso zovala zaubweya wa nkhosa zamtundu wapepo zimene mafumu a Midiyani aja anavala, osawerengeranso mikanda imene inali mʼkhosi mwa ngamila zawo.+
-