Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ‘Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ine ndichititsa zida zankhondo zimene zili mʼmanja mwanu kukutembenukirani. Zimenezi ndi zida zimene mukugwiritsa ntchito pomenyana ndi mfumu ya Babulo+ ndi Akasidi amene akuzungulirani kunja kwa mpanda wanu. Ndipo ine ndidzasonkhanitsa zidazo pakati pa mzindawu.

  • Ezekieli 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma kenako mfumu ya Yuda inapandukira mfumu ya Babulo+ potumiza amithenga ku Iguputo kuti akatenge mahatchi+ ndi gulu lalikulu la asilikali.+ Kodi zinthu zidzaiyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi angapewe chilango? Kodi angaphwanye pangano nʼkupewabe chilango?’+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani