2 Mafumu 25:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+ 2 Mbiri 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inatentha nyumba ya Mulungu woona,+ kugwetsa mpanda wa Yerusalemu,+ kutentha nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndiponso zinthu zonse zamtengo wapatali.+ Maliro 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wasonyeza ukali wake.Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+ Ndipo iye wayatsa moto mʼZiyoni, umene wawotcha maziko ake.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ mʼnyumba yopatulika.+ Sinamvere chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena wodwala.+ Mulungu anapereka zonse mʼmanja mwake.+
19 Inatentha nyumba ya Mulungu woona,+ kugwetsa mpanda wa Yerusalemu,+ kutentha nyumba zonse zokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndiponso zinthu zonse zamtengo wapatali.+
11 Yehova wasonyeza ukali wake.Wakhuthula mkwiyo wake woyaka moto.+ Ndipo iye wayatsa moto mʼZiyoni, umene wawotcha maziko ake.+