-
Yeremiya 32:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Pa nthawi imeneyo, asilikali a mfumu ya Babulo anali atazungulira Yerusalemu. Ndipo mneneri Yeremiya anali atamutsekera mʼnyumba imene inali mʼBwalo la Alonda,+ limene linali pafupi ndi nyumba ya mfumu ya Yuda.
-
-
Yeremiya 33:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Yeremiya adakali mʼBwalo la Alonda+ momwe anamutsekera, Yehova analankhula naye kachiwiri kuti:
-
-
Yeremiya 38:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 ndipo iwo anakoka Yeremiya ndi zingwezo nʼkumutulutsa mʼchitsimemo. Yeremiya anapitiriza kukhala mʼBwalo la Alonda.+
-