Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 16:23, 24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Omuri anakhala mfumu ya Isiraeli mʼchaka cha 31 cha Asa mfumu ya Yuda ndipo analamulira zaka 12. Ku Tiriza analamulirako zaka 6. 24 Iye anagula phiri la Samariya kwa Semeri ndi matalente* awiri asiliva ndipo anamanga mzinda paphiripo. Mzindawo anaupatsa dzina lakuti Samariya*+ lomwe linali dzina la Semeri, mwiniwake* wa phirilo.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani