-
Yeremiya 44:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Akaziwo anawonjezera kuti: “Ndipo pamene tinkapereka nsembe ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa Mfumukazi Yakumwamba,* kodi amuna athu sanavomereze kuti tipangire Mfumukaziyo makeke oti tikapereke nsembe opangidwa mʼchifanizo chake ndiponso kuti tipereke kwa iye nsembe zachakumwazo?”
-