Ezekieli 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononganso mafano onyansa* nʼkuthetsa milungu yopanda pake ya ku Nofi.*+ Sipadzapezekanso kalonga* wochokera mʼdziko la Iguputo ndipo ndidzachititsa kuti anthu amʼdzikolo azikhala mwamantha.+
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononganso mafano onyansa* nʼkuthetsa milungu yopanda pake ya ku Nofi.*+ Sipadzapezekanso kalonga* wochokera mʼdziko la Iguputo ndipo ndidzachititsa kuti anthu amʼdzikolo azikhala mwamantha.+