Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yeremiya 25:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova Mulungu wa Isiraeli anandiuza kuti: “Tenga kapu iyi ya vinyo wa mkwiyo imene ili mʼdzanja langa ndipo ukamwetse mitundu yonse imene ndikukutumizako.

  • Yeremiya 25:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako ndinamwetsanso Farao mfumu ya Iguputo, atumiki ake, akalonga ake ndi anthu ake onse+

  • Ezekieli 29:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana kwa Farao mfumu ya Iguputo ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+

  • Ezekieli 32:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira yokhudza Farao, mfumu ya Iguputo ndipo umuuze kuti,

      ‘Iwe unali ngati mkango waungʼono wamphamvu* wa mitundu ina ya anthu,

      Koma wakhalitsidwa chete.

      Unali ngati chilombo chamʼnyanja+ chimene chimavundula madzi mwamphamvu mʼmitsinje yako

      Nʼkumadetsa madzi ndi mapazi ako ndiponso kuipitsa mitsinjeyo.’

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani