Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ezekieli 26:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, Turo wanena Yerusalemu+ kuti, ‘Eyaa! Zakhala bwino. Mzinda umene unkakopa anthu a mitundu ina wathyoledwa.+ Tsopano zinthu zindiyendera bwino ndipo ndilemera chifukwa mzindawo wawonongedwa.’

  • Amosi 1:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Yehova wanena kuti,

      ‘Popeza Turo anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.

      Chifukwa anapereka ku Edomu gulu lonse la anthu ogwidwa ukapolo,

      Ndiponso chifukwa chakuti sanakumbukire pangano la pachibale.+

      10 Choncho ndidzatumiza moto pampanda wa Turo,

      Ndipo udzawotcheratu nsanja zake zolimba.’+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani