-
Numeri 24:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ndidzamuona, koma osati panopa;
Ndidzamupenya, koma osati posachedwa.
Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+
Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza.
-