Yesaya 47:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano imva izi, iwe amene umakonda zosangalatsa,+Amene umakhala motetezeka, iwe amene umanena mumtima mwako kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.+ Sindidzakhala wamasiye Ndipo ana anga sadzafa.”+
8 Tsopano imva izi, iwe amene umakonda zosangalatsa,+Amene umakhala motetezeka, iwe amene umanena mumtima mwako kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.+ Sindidzakhala wamasiye Ndipo ana anga sadzafa.”+