-
Yeremiya 23:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 “Tsoka abusa amene akuwononga ndi kubalalitsa nkhosa zapamalo anga odyetsera ziweto!” akutero Yehova.+
-
-
Ezekieli 34:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho zinamwazikana chifukwa zinalibe mʼbusa+ ndipo zinakhala chakudya cha zilombo zonse zakutchire.
-