-
Yesaya 14:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 “Ine ndidzawaukira,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
“Ndipo mʼBabulo ndidzachotsamo dzina, anthu otsala, ana komanso mbadwa,”+ akutero Yehova.
23 “Babulo ndidzamusandutsa malo okhala nungu* ndiponso malo a zithaphwi. Ndidzamusesa ndi tsache la chiwonongeko,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-