-
Yesaya 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Anthu apanikizika.+
Nsautso ndi zowawa zawagwera
Ngati mkazi amene akubereka.
Akuyangʼanana mwamantha,
Ndipo nkhope zawo zikuonekeratu kuti ali ndi nkhawa.
-