Yesaya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yeremiya 50:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+Ndipo anthu ake amachita zinthu ngati amisala chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha. Chivumbulutso 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
38 Madzi ake adzawonongedwa ndipo adzauma.+ Dziko limeneli ndi la zifaniziro zogoba,+Ndipo anthu ake amachita zinthu ngati amisala chifukwa cha masomphenya awo ochititsa mantha.