Yesaya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+ Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
20 Tulukani mʼBabulo!+ Thawani mʼmanja mwa Akasidi. Lengezani zimenezi mofuula komanso mosangalala. Uzani anthu zimenezi.+ Zineneni kuti anthu azidziwe mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Munene kuti: “Yehova wawombola mtumiki wake Yakobo.+